Welcome to our channel...We provide well detailed news,analysis and well researched commentaries and up-to-date stories around the country and beyond..Stay updated on political, entertainment and trending topics.
Bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) lakweza mitengo ya mafuta a galimoto kuyambira Lero pa 1 April.
Mafuta apetulo tsopano adzigulitsidwa pa mtengo wa k6672 pa litre kuchoka pa mtengo wa k4965 pa litre pomwe mafuta a dizilo achoka pa mtengo wa k4945 kufika pa k 6687.
Yemwe anali mlembi muofesi ya President ndi nduna a Colleen Zamba agonaso ku polisi kaamba koti apolisi alephera kuwatengera ku bwalo lamilandu lero kuti amve mulandu omwe awapatsa komanso kupempha belo.
Izi zachitika masana ano pomwe ngakhale apolisiwa anali atanyamuka ndi a Zamba kubwera kubwaloli ati alandira uthenga kuti abwelere kupolisi.
Loya wa a Zamba, a Sylvester Ayuba James wati auzidwa kuti a Zamba abwelera nawo atatsara pang'ono kufika kubwalo kaamba koti kwatsala maola ena mumaola 48 omwe amalola apolisiwa kusunga munthu.
Iwo ati ndiokhumudwa ndizomwe zachitikazi potsindika kuti akuona kuti apolisiwa akufuna kuzunza chabe a Zamba.
A Ayuba James aululaso kuti apolisi awaonetsa chilolezo chabwalo lamilandu chakuti afufuze mulamya za a Colleen Zamba koma ati sanawafotokozere zomwe akufuna kuona mulamyazi.
Bungwe loona zamphamvu la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) lalengeza za kukwera mtengo wa mafuta a galimoto m'dziko lino kuyambira lero. Petrol adzigulitsa pamtengo wa K3,499 pa lita kuchoka pa K2,530 kuimira 38.30%.
Kalata yomwe a MERA atulutsa yomwe wasainira ndi wapampando wa board ya bungweli, a Charles Kambauwa, mtengo wa diesel wakwera ndi 28.02% kuchoka K2,734 kufika pa K3,500 pa lita.
Chipani cha DPP chatemetsa nkhwangwa pa mwala kuti mtsogoleri wake Peter Mutharika sakhala nawo pa mtsutso womwe ulipo lero.
Mneneli wa chipanichi a Shadric Namalomba ati chipanichi sichikusintha za ganizo lakeli.
Izi zili chomwechi pomwe komiti yomwe yakonza mtsutso-wu yati ikufunitsitsabe kuti zipani za DPP komanso MCP zitenge nawo gawo pa mtsutso wa lero.
Pa mtsutso womwe udachitika mwezi wapitawu, zipani za UTM, UDF ndi PP ndi zomwe zidatenga nawo gawo.
Koma wachiwiri kwa mneneli wa chipani cha MCP Ken Msonda wati chipanichi pakadali chili kalikiliki kuchititsa misonkhano yokopa anthu ndiye nkovuta kuti mtsogoleri wake apezeke kumeneku.
Usiku wa lero dziko la Malawi likumana ndi kadausiku wa mwezi pamene dziko liri pakati pa dzuwa ndi mwezi.
Izi zimachitika pomwe mwezi wafika theka la ulendo wake wozungulira dziko.
Izi zikupangitsa kuti dziko litsitire kuwala kuchoka ku dzuwa kupita ku mwezi choncho zikupangitsa kuti pakhale kamdima pa mwezi ndipo mwezi suwala bwinobwino.
The Department of Immigration and Citizenship Services has reaffirmed its commitment to help people apply for and get their passports.
The Department's national spokesperson, Pasqually Zulu, has said this responding to a story of the temporal suspension of passport applications, which has been issued through a statement under The Malawi High Commission in London.
Zulu says while they value the efforts done by the diaspora community in enhancing social economic development of the country, all passport submission and processing services are still operational in all embassies.
He therefore called all Malawians to continue applying for their passports, saying the Department is still using onsite applications which are physical.
"For now, we are now done with the on-site system installation in all regions, service seekers are enjoying the service, we will now roll out the system to 6 strategic districts which will be followed by online system activation which will also involve all embassies to allow applicants to apply passports in the comfort of thier homes" Zulu said.
Malawi Daily Voice
Bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority
(MERA) lakweza mitengo ya mafuta a galimoto kuyambira Lero pa 1 April.
Mafuta apetulo tsopano adzigulitsidwa pa mtengo wa
k6672 pa litre kuchoka pa mtengo wa k4965 pa litre pomwe mafuta a dizilo achoka pa mtengo wa k4945 kufika pa k 6687.
1 week ago | [YT] | 26
View 0 replies
Malawi Daily Voice
Breaking news !!
Richard Chimwendo Banda wakazipeleka yekha ku headquarters ya police ku Lilongwe.
Tikupasilani zambiri
3 months ago | [YT] | 24
View 2 replies
Malawi Daily Voice
#Nkhani
Yemwe anali mlembi muofesi ya President ndi nduna a Colleen Zamba agonaso ku polisi kaamba koti apolisi alephera kuwatengera ku bwalo lamilandu lero kuti amve mulandu omwe awapatsa komanso kupempha belo.
Izi zachitika masana ano pomwe ngakhale apolisiwa anali atanyamuka ndi a Zamba kubwera kubwaloli ati alandira uthenga kuti abwelere kupolisi.
Loya wa a Zamba, a Sylvester Ayuba James wati auzidwa kuti a Zamba abwelera nawo atatsara pang'ono kufika kubwalo kaamba koti kwatsala maola ena mumaola 48 omwe amalola apolisiwa kusunga munthu.
Iwo ati ndiokhumudwa ndizomwe zachitikazi potsindika kuti akuona kuti apolisiwa akufuna kuzunza chabe a Zamba.
A Ayuba James aululaso kuti apolisi awaonetsa chilolezo chabwalo lamilandu chakuti afufuze mulamya za a Colleen Zamba koma ati sanawafotokozere zomwe akufuna kuona mulamyazi.
4 months ago | [YT] | 6
View 3 replies
Malawi Daily Voice
#Breaking_News
Mtsogoleri wadziko lino Proffesor Arthur Peter Mutharika walengeza kuti Thumba la Feteleza anthu azigura k10 thousand pa ndondomeko ija ya FISP Ndipo anthu azipasidwa Mbeu yaulere yaku Mtima Kwawo.
#Parliament_Opening_Ceremony
5 months ago | [YT] | 108
View 5 replies
Malawi Daily Voice
#NKHANI
Bungwe loona zamphamvu la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) lalengeza za kukwera mtengo wa mafuta a galimoto m'dziko lino kuyambira lero. Petrol adzigulitsa pamtengo wa K3,499 pa lita kuchoka pa K2,530 kuimira 38.30%.
Kalata yomwe a MERA atulutsa yomwe wasainira ndi wapampando wa board ya bungweli, a Charles Kambauwa, mtengo wa diesel wakwera ndi 28.02% kuchoka K2,734 kufika pa K3,500 pa lita.
6 months ago | [YT] | 25
View 1 reply
Malawi Daily Voice
NKHANI
Mwambo olumbiritsa mtsogoleri watsopano wadziko lino a Peter Mutharika uchitika loweruka likudzali pabwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre.
Mneneri wa a Mutharika a Shadric Namalomba watsimikiza za izi ngakhale sanafotokoze zambiri zankhaniyi.
6 months ago | [YT] | 100
View 4 replies
Malawi Daily Voice
BREAKING NEWS
Mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera wavomeleza kulephera kwake pa chisankho cha President cha pa September 16.
A Chakwera ayamikira ndikufunira zabwino mtsogoleri wa DPP a Peter Mutharika kaamba kakupambana kwawo pa chisankhochi.
Iwo ati ndiokhonzeka kupeleka Boma mwamtendere
6 months ago | [YT] | 39
View 12 replies
Malawi Daily Voice
#NKHANI
Chipani cha DPP chatemetsa nkhwangwa pa mwala kuti mtsogoleri wake Peter Mutharika sakhala nawo pa mtsutso womwe ulipo lero.
Mneneli wa chipanichi a Shadric Namalomba ati chipanichi sichikusintha za ganizo lakeli.
Izi zili chomwechi pomwe komiti yomwe yakonza mtsutso-wu yati ikufunitsitsabe kuti zipani za DPP komanso MCP zitenge nawo gawo pa mtsutso wa lero.
Pa mtsutso womwe udachitika mwezi wapitawu, zipani za UTM, UDF ndi PP ndi zomwe zidatenga nawo gawo.
Koma wachiwiri kwa mneneli wa chipani cha MCP Ken Msonda wati chipanichi pakadali chili kalikiliki kuchititsa misonkhano yokopa anthu ndiye nkovuta kuti mtsogoleri wake apezeke kumeneku.
*📘MDV NEWS UPDATE*
6 months ago | [YT] | 37
View 12 replies
Malawi Daily Voice
#NKHANI
Usiku wa lero dziko la Malawi likumana ndi kadausiku wa mwezi pamene dziko liri pakati pa dzuwa ndi mwezi.
Izi zimachitika pomwe mwezi wafika theka la ulendo wake wozungulira dziko.
Izi zikupangitsa kuti dziko litsitire kuwala kuchoka ku dzuwa kupita ku mwezi choncho zikupangitsa kuti pakhale kamdima pa mwezi ndipo mwezi suwala bwinobwino.
7 months ago | [YT] | 13
View 6 replies
Malawi Daily Voice
*MDV NEWS
The Department of Immigration and Citizenship Services has reaffirmed its commitment to help people apply for and get their passports.
The Department's national spokesperson, Pasqually Zulu, has said this responding to a story of the temporal suspension of passport applications, which has been issued through a statement under The Malawi High Commission in London.
Zulu says while they value the efforts done by the diaspora community in enhancing social economic development of the country, all passport submission and processing services are still operational in all embassies.
He therefore called all Malawians to continue applying for their passports, saying the Department is still using onsite applications which are physical.
"For now, we are now done with the on-site system installation in all regions, service seekers are enjoying the service, we will now roll out the system to 6 strategic districts which will be followed by online system activation which will also involve all embassies to allow applicants to apply passports in the comfort of thier homes" Zulu said.
7 months ago | [YT] | 9
View 1 reply
Load more